Mpaka Udzipita lyrics by Langwan Piksy - original song full text. Official Mpaka Udzipita lyrics, 2024 version | LyricsMode.com
Request & respond explanations
  • Don't understand the meaning of the song?
  • Highlight lyrics and request an explanation.
  • Click on highlighted lyrics to explain.
Langwan Piksy – Mpaka Udzipita lyrics
Ndikudziwa kuti ndafika mammawa
Ndikudziwa zaku bhowa
Yeah mtima wako ukuwawa
Koma babe ukudziwa za ku bhawa

Ndimakupeza wagona
Sticheza ngati banja
Ine Ndimakhala ndatopa
Lonseli ndi vuto langa

Mammawa uliwonse ukumalira
Lero Ndakupeza ukupakila
Komano honey just hold on
I know I've done wrong
Komazi ndi zazing'ono
Nde

CHORUS
Mpaka udzipita
Sindufuna kusikidwa.
Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa

Yes I know I didn't give you much attention
Lately
Every time on the cellphone
Too much what'sapp, too much twitter
Umafuna kundikonda koma sinkupasa mita
Busy ntchito weekend ndi anzanga
Ndimalonjeza zinthu zochuluka simpanga
Umadandaula koma mmaiwala nsanga
Kuchitenga for granted chikondi chomwe umandipatsa
Mmalo molowera mmwamba I know we going down
Ndikale lomwe ndinayenda nawe mtown
Komano honey just hold on
I know I'm doing wrong
Komazi ndi zazing'ono
Nde

CHORUS
Mpaka udzipita
Sindufuna kusikidwa.
Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa

Usayese ndikutenga simple
Kwa ine utanthauza dziko
Chikondi chako chindipasa dzitho
Ndikamati ndine mphongo ndiwe

I swallow my pride ndameza matama
Ndameza zochuluka pa kamoz
Ndatsamwa
Ndiri ndi munda koma sinkupalira
Ndikudziwa sukukondwa mmomwe zikukhalira

Ndiwauza anzanga ino weekend
Sindioneka poti ndikhala ndiwe
Eh yah ndikhala ndiwe baby
Sindilora upite

CHORUS
Mpaka udzipita
Sindufuna kusikidwa.
Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa
×



Lyrics taken from /lyrics/l/langwan_piksy/mpaka_udzipita.html

  • Email
  • Correct
Submitted by Langwan_Piksy

Mpaka Udzipita meanings

Write about your feelings and thoughts about Mpaka Udzipita

Know what this song is about? Does it mean anything special hidden between the lines to you? Share your meaning with community, make it interesting and valuable. Make sure you've read our simple tips.
U
Min 50 words
Not bad
Good
Awesome!

Post meanings

U
Min 50 words
Not bad
Good
Awesome!

Featured lyrics

0-9 A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z